2 Mbiri 35:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atumiki akewo anamutsitsa mʼgaletalo nʼkumukweza mʼgaleta lake lina lankhondo ndipo anabwerera naye ku Yerusalemu. Iye anafa ndipo anamuika mʼmanda a makolo ake.+ Ayuda onse ndi anthu onse a ku Yerusalemu analira maliro a Yosiya.
24 Atumiki akewo anamutsitsa mʼgaletalo nʼkumukweza mʼgaleta lake lina lankhondo ndipo anabwerera naye ku Yerusalemu. Iye anafa ndipo anamuika mʼmanda a makolo ake.+ Ayuda onse ndi anthu onse a ku Yerusalemu analira maliro a Yosiya.