-
Ezara 5:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Izi nʼzimene zinali mʼkalata imene Tatenai bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje, Setara-bozenai ndi anzake ndiponso abwanamkubwa aangʼono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo.
-