Ezara 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Izi n’zimene zinali m’kalata+ imene Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzake,+ ndiponso abwanamkubwa aang’ono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo. Ezara Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 3 2017, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,6/15/1993, tsa. 32
6 Izi n’zimene zinali m’kalata+ imene Tatenai+ bwanamkubwa wa kutsidya lina la Mtsinje,+ Setara-bozenai+ ndi anzake,+ ndiponso abwanamkubwa aang’ono amene anali kutsidya lina la Mtsinje, anatumiza kwa mfumu Dariyo.