Ezara 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma chifukwa chakuti makolo athu anakwiyitsa Mulungu wakumwamba,+ iye anawapereka mʼmanja mwa Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo Mkasidi, yemwe anagwetsa nyumbayi+ nʼkutenga anthu kupita nawo ku ukapolo ku Babulo.+
12 Koma chifukwa chakuti makolo athu anakwiyitsa Mulungu wakumwamba,+ iye anawapereka mʼmanja mwa Nebukadinezara+ mfumu ya Babulo Mkasidi, yemwe anagwetsa nyumbayi+ nʼkutenga anthu kupita nawo ku ukapolo ku Babulo.+