-
Ezara 5:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Tsopano ngati inu mfumu mukuona kuti nʼkoyenera, uzani anthu kuti afufuze mʼnyumba ya chuma cha mfumu imene ili ku Babuloko. Muwauze kuti aone ngati mfumu Koresi inaikadi lamulo loti nyumba ya Mulungu yomwe ili ku Yerusalemu+ imangidwenso. Kenako inu mfumu mutitumizire chigamulo chanu pa nkhani imeneyi.”
-