Nehemiya 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense amene ankamanga, anali atamangirira lupanga mʼchiuno ndipo woliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa anaima pafupi ndi ine. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:18 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 9
18 Aliyense amene ankamanga, anali atamangirira lupanga mʼchiuno ndipo woliza lipenga la nyanga+ ya nkhosa anaima pafupi ndi ine.