Nehemiya 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Aliyense wa omangawo anali atamangirira lupanga lake m’chiuno+ pamene anali kumanga+ mpandawo, ndipo munthu woliza lipenga la nyanga ya nkhosa+ anali pambali panga. Nehemiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:18 Nsanja ya Olonda,2/1/2006, tsa. 9
18 Aliyense wa omangawo anali atamangirira lupanga lake m’chiuno+ pamene anali kumanga+ mpandawo, ndipo munthu woliza lipenga la nyanga ya nkhosa+ anali pambali panga.