Numeri 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Adani okuvutitsani akakuukirani+ kuti akuthireni nkhondo m’dziko lanu, muziliza malipengawo+ moitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Mulungu wanu Yehova adzakukumbukirani ndithu ndi kukupulumutsani kwa adani anuwo.+ 2 Mbiri 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Taonani, ife patsogolo pathu pali Mulungu woona+ ndi ansembe ake,+ ndi malipenga+ otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu ana a Isiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu,+ chifukwa simupambana.”+ Miyambo 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+
9 “Adani okuvutitsani akakuukirani+ kuti akuthireni nkhondo m’dziko lanu, muziliza malipengawo+ moitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Mulungu wanu Yehova adzakukumbukirani ndithu ndi kukupulumutsani kwa adani anuwo.+
12 Taonani, ife patsogolo pathu pali Mulungu woona+ ndi ansembe ake,+ ndi malipenga+ otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu ana a Isiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu,+ chifukwa simupambana.”+
18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+