Numeri 23:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake. Deuteronomo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+ Salimo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
21 Iye sanaone mphamvu yamatsenga+ iliyonse ikuchita kanthu pa Yakobo,Ndipo sanaone Isiraeli akuponyeredwa vuto.Mulungu wake Yehova ali naye,+Ndipo mfuu yotamanda mfumu ikumveka pakati pake.
4 chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyenda limodzi nanu kuti akumenyereni nkhondo ndi kukupulumutsani kwa adani anu.’+
7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+