Yobu 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena kodi uli ndi dzanja ngati la Mulungu woona?+Kodi ungachititse mabingu kugunda ndi mawu ngati a Mulungu?+ Yesaya 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko, ndipo kwa iye ili ngati fumbi pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba+ ngati kuti ndi fumbi. Aheberi 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kulandira chilango chochokera kwa Mulungu wamoyo n’chinthu choopsa.+
9 Kapena kodi uli ndi dzanja ngati la Mulungu woona?+Kodi ungachititse mabingu kugunda ndi mawu ngati a Mulungu?+
15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko, ndipo kwa iye ili ngati fumbi pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba+ ngati kuti ndi fumbi.