Yobu 37:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pambuyo pake pamamveka phokoso.Iye amabangula+ ndi mawu ake amphamvu.+Mawu ake akamveka, iye saletsa mphezizo.+ Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
4 Pambuyo pake pamamveka phokoso.Iye amabangula+ ndi mawu ake amphamvu.+Mawu ake akamveka, iye saletsa mphezizo.+
3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+