Yobu 40:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kapena kodi uli ndi dzanja ngati la Mulungu woona?+Kodi ungachititse mabingu kugunda ndi mawu ngati a Mulungu?+ Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
9 Kapena kodi uli ndi dzanja ngati la Mulungu woona?+Kodi ungachititse mabingu kugunda ndi mawu ngati a Mulungu?+
3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+