Ekisodo 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+ Salimo 89:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mkono wamphamvu ndi wanu,+Dzanja lanu ndi lamphamvu,+Dzanja lanu lamanja ndi lokwezeka.+ 1 Akorinto 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapena “kodi tikufuna kuputa nsanje+ ya Yehova”? Kodi mphamvu zathu zingafanane ndi zake?+
6 Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, likusonyeza kupambana kwa mphamvu zake.+Dzanja lanu lamanja, inu Yehova, limaphwanya mdani.+