-
Nehemiya 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho ndinawauza kuti: “Mageti a Yerusalemu sayenera kutsegulidwa mpaka dzuwa litakwera. Alonda amʼmageti aime pafupi ndipo atseke zitseko nʼkuzikhoma ndi anamphatika. Muikenso alonda a anthu a ku Yerusalemu, ena muwaike pamalo awo olondera ndipo ena muwaike kutsogolo kwa nyumba zawo.”
-