-
Nehemiya 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho ndinawauza kuti: “Zipata+ za Yerusalemu siziyenera kutsegulidwa kufikira dzuwa litatentha. Alonda a m’zipatazo atseke zitseko ndi kuzikhoma ndi akapichi ndipo aime pafupi.+ Muikenso alonda a anthu okhala mu Yerusalemu, ena muwaike pamalo awo olondera ndipo ena muwaike kutsogolo kwa nyumba zawo.”+
-