Nehemiya 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mzindawo unali wotakasuka ndiponso waukulu. Munali anthu ochepa+ ndipo nyumba zinali zisanamangidwenso.
4 Mzindawo unali wotakasuka ndiponso waukulu. Munali anthu ochepa+ ndipo nyumba zinali zisanamangidwenso.