Nehemiya 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano mzindawo unali wotakasuka ndi waukulu. Mkati mwake munali anthu ochepa+ ndipo sanamangemo nyumba.
4 Tsopano mzindawo unali wotakasuka ndi waukulu. Mkati mwake munali anthu ochepa+ ndipo sanamangemo nyumba.