Nehemiya 7:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Apa sanawerengere akapolo awo aamuna ndi akapolo awo aakazi+ amene analipo 7,337. Iwo analinso ndi oimba aamuna ndi aakazi 245.+
67 Apa sanawerengere akapolo awo aamuna ndi akapolo awo aakazi+ amene analipo 7,337. Iwo analinso ndi oimba aamuna ndi aakazi 245.+