Yobu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana ake ndi osatetezeka,Ndipo amaponderezedwa pageti la mzinda,+ popanda wowapulumutsa.