Yobu 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana ake amakhala kutali ndi chipulumutso,+Ndipo amaponderezedwa pachipata, popanda wowapulumutsa.