Salimo 109:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mbadwa zake ziphedwe ndi kuchotsedwa m’dziko.+Dzina lawo lifafanizidwe mu m’badwo wotsatira.+ Salimo 119:155 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 155 Chipulumutso chili kutali ndi anthu oipa,+Pakuti sanaphunzire malamulo anu ndi kuwasunga.+