Salimo 119:155 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 155 Chipulumutso chili kutali kwambiri ndi anthu oipa,Chifukwa sanaphunzire malamulo anu.+