Salimo 119:155 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 155 Chipulumutso chili kutali ndi anthu oipa,+Pakuti sanaphunzire malamulo anu ndi kuwasunga.+