Salimo 73:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti onse okhala kutali ndi inu adzatheratu.+Mudzawononga ndithu aliyense wochita chigololo mwa kukusiyani.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+
27 Pakuti onse okhala kutali ndi inu adzatheratu.+Mudzawononga ndithu aliyense wochita chigololo mwa kukusiyani.+