-
Yobu 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Bwenzi atakuululira chinsinsi cha nzeru,
Chifukwa pali zambiri zofunika kuziphunzira zokhudza nzeru yeniyeni.
Bwenzi utazindikira kuti Mulungu walola kuti zolakwa zako zina ziiwalike.
-