Yobu 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Bwenzi atakuuza chinsinsi cha nzeru,Chifukwa zinthu za nzeru ndiponso zopindulitsa n’zambiri.Komanso bwenzi utadziwa kuti Mulungu wachititsa kuti zolakwa zako zina ziiwalike.+
6 Bwenzi atakuuza chinsinsi cha nzeru,Chifukwa zinthu za nzeru ndiponso zopindulitsa n’zambiri.Komanso bwenzi utadziwa kuti Mulungu wachititsa kuti zolakwa zako zina ziiwalike.+