Yobu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inde, kuwala kwa woipa kudzazimitsidwa,Ndipo malawi a moto wake sadzawala.+