Yobu 8:13, 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha,14 Anthu amene amadalira zinthu zosathandiza,Amene amadalira zinthu zosalimba ngati ulusi wa kangaude.* Yobu 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma maso a anthu oipa sadzaonanso,Ndipo sadzapeza malo othawirako,Chiyembekezo chawo chidzakhala imfa* basi.”+
13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha,14 Anthu amene amadalira zinthu zosathandiza,Amene amadalira zinthu zosalimba ngati ulusi wa kangaude.*
20 Koma maso a anthu oipa sadzaonanso,Ndipo sadzapeza malo othawirako,Chiyembekezo chawo chidzakhala imfa* basi.”+