Yobu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndi mmene zilili njira za onse oiwala Mulungu,+Ndipo chiyembekezo cha wampatuko chidzatha.+