Yobu 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye watseka njira yanga ndi khoma lamiyala moti sindingathe kudutsa,Watchinga njira zanga ndi mdima.+
8 Iye watseka njira yanga ndi khoma lamiyala moti sindingathe kudutsa,Watchinga njira zanga ndi mdima.+