Yobu 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kodi nyale ya oipa imazimitsidwa kangati?+ Ndipo tsoka limawagwera kangati? Kodi Mulungu amawawononga kangati atakwiya?
17 Kodi nyale ya oipa imazimitsidwa kangati?+ Ndipo tsoka limawagwera kangati? Kodi Mulungu amawawononga kangati atakwiya?