Yobu 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu amasuntha zizindikiro za malire.+Iwo amaba ziweto nʼkuzipititsa pamalo awo odyetsera ziweto.