Yobu 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali ena amene amapandukira kuwala.+Iwo sazindikira njira zake,Ndipo sayenda mʼnjira zake.