Yobu 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Oipawo amasonyeza kuti ali pakati pa opanduka omwe amatsutsana ndi kuwala.+Iwo sanazindikire njira zake,Ndipo sanakhale m’misewu yake.
13 Oipawo amasonyeza kuti ali pakati pa opanduka omwe amatsutsana ndi kuwala.+Iwo sanazindikire njira zake,Ndipo sanakhale m’misewu yake.