Yobu 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo amalira kuti athandizidwe, koma iye sawayankha,+Chifukwa cha kunyada kwa anthu oipa.+