Salimo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kudzera mʼmawu otamanda ochokera mʼkamwa mwa ana ndi mwa makanda+Mwasonyeza mphamvu zanu chifukwa cha adani anu,Kuti adani anu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa akhale chete. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 101-102 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
2 Kudzera mʼmawu otamanda ochokera mʼkamwa mwa ana ndi mwa makanda+Mwasonyeza mphamvu zanu chifukwa cha adani anu,Kuti adani anu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa akhale chete.