Salimo 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 101-102 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
2 M’kamwa mwa ana aang’ono ndi ana oyamwa mwakhazikitsamo zamphamvu,+Chifukwa cha amene akukuchitirani zoipa.+Mwatero kuti mugonjetse mdani wanu komanso amene akufuna kukubwezerani zoipa.+