Salimo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Malo amene andiyezera ndi abwino kwambiri. Inde, ndikukhutira ndi cholowa chimene ndapatsidwa.+