Salimo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zingwe zoyezera zandigwera m’malo abwino.+Ndithudi, gawo limene ndapatsidwa ndalivomereza.