Salimo 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amandigoneka mʼmalo odyetsera ziweto a msipu wambiri.Amanditsogolera kumalo opumira a madzi ambiri.*+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:2 Nsanja ya Olonda,11/1/2005, ptsa. 17-189/15/2002, tsa. 327/1/1988, tsa. 24
2 Amandigoneka mʼmalo odyetsera ziweto a msipu wambiri.Amanditsogolera kumalo opumira a madzi ambiri.*+