Salimo 39:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinakhala chete osalankhula kanthu.+Sindinalankhule kanthu ngakhale kokhudza zinthu zabwino,Koma ululu wanga unali waukulu.
2 Ndinakhala chete osalankhula kanthu.+Sindinalankhule kanthu ngakhale kokhudza zinthu zabwino,Koma ululu wanga unali waukulu.