Salimo 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atsogoleri a mitundu ya anthu asonkhana pamodziNdi anthu a Mulungu wa Abulahamu. Chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu pa olamulira a* dziko lapansi. Iye ndi wokwezeka kwambiri.+
9 Atsogoleri a mitundu ya anthu asonkhana pamodziNdi anthu a Mulungu wa Abulahamu. Chifukwa Mulungu ali ndi mphamvu pa olamulira a* dziko lapansi. Iye ndi wokwezeka kwambiri.+