Salimo 47:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atsogoleri a mitundu ya anthu asonkhana.+Asonkhana pamodzi ndi anthu a Mulungu wa Abulahamu.+Pakuti anthu onse omwe ali ngati zishango* za dziko lapansi ndi a Mulungu.+Iye wakwera pamalo okwezeka kwambiri.+
9 Atsogoleri a mitundu ya anthu asonkhana.+Asonkhana pamodzi ndi anthu a Mulungu wa Abulahamu.+Pakuti anthu onse omwe ali ngati zishango* za dziko lapansi ndi a Mulungu.+Iye wakwera pamalo okwezeka kwambiri.+