Salimo 58:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Miphika yanu isanayambe kumva kutentha kwa moto wa mitengo yaminga,Mulungu adzauluza mitengo yaiwisi komanso imene ikuyaka ngati ikuuluzika ndi mphepo yamkuntho.+
9 Miphika yanu isanayambe kumva kutentha kwa moto wa mitengo yaminga,Mulungu adzauluza mitengo yaiwisi komanso imene ikuyaka ngati ikuuluzika ndi mphepo yamkuntho.+