Salimo 68:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamisonkhano tamandani Mulungu,Tamandani Yehova, inu nonse amene moyo wanu ukuchokera mu Kasupe wa Isiraeli.+
26 Pamisonkhano tamandani Mulungu,Tamandani Yehova, inu nonse amene moyo wanu ukuchokera mu Kasupe wa Isiraeli.+