Salimo 68:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Dzudzulani nyama zakutchire zimene zimakhala mʼmabango,Gulu la ngʼombe zamphongo+ limodzi ndi ana awo,Mpaka mitundu ya anthu itagwada nʼkubweretsa ndalama zasiliva. Koma iye wabalalitsa mitundu ya anthu imene imasangalala ndi nkhondo. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 68:30 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 10
30 Dzudzulani nyama zakutchire zimene zimakhala mʼmabango,Gulu la ngʼombe zamphongo+ limodzi ndi ana awo,Mpaka mitundu ya anthu itagwada nʼkubweretsa ndalama zasiliva. Koma iye wabalalitsa mitundu ya anthu imene imasangalala ndi nkhondo.