Salimo 68:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Dzudzulani nyama yakutchire yokhala m’mabango,+ gulu la ng’ombe zamphongo,+Pamodzi ndi mitundu ya anthu imene ili ngati ana a ng’ombe amphongo, aliyense amene akupondaponda ndalama zasiliva.+Iye wabalalitsa mitundu ya anthu yokonda ndewu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 68:30 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, tsa. 10
30 Dzudzulani nyama yakutchire yokhala m’mabango,+ gulu la ng’ombe zamphongo,+Pamodzi ndi mitundu ya anthu imene ili ngati ana a ng’ombe amphongo, aliyense amene akupondaponda ndalama zasiliva.+Iye wabalalitsa mitundu ya anthu yokonda ndewu.+