2 Samueli 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene Asiriya a ku Damasiko+ anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.+ Salimo 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+ Ezekieli 39:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+
5 Pamene Asiriya a ku Damasiko+ anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.+
12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+
18 Mudzadya mnofu wa anthu amphamvu,+ mudzamwa magazi a atsogoleri a dziko lapansi, nkhosa zamphongo, ana a nkhosa amphongo,+ mbuzi zamphongo ndi ng’ombe zamphongo.+ Zonsezi ndi nyama zonenepa za ku Basana.+