1 Mafumu 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide atapha+ anthu a ku Zoba, Rezoni anayamba kusonkhanitsa anthu kumbali yake, ndipo anakhala mtsogoleri wa gulu la achifwamba. Chotero iye ndi gulu lakelo anapita kukakhala ku Damasiko,+ n’kuyamba kulamulira kumeneko. Yesaya 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+
24 Davide atapha+ anthu a ku Zoba, Rezoni anayamba kusonkhanitsa anthu kumbali yake, ndipo anakhala mtsogoleri wa gulu la achifwamba. Chotero iye ndi gulu lakelo anapita kukakhala ku Damasiko,+ n’kuyamba kulamulira kumeneko.
8 Pakuti mutu wa Siriya ndiwo Damasiko, ndipo mutu wa Damasiko ndiwo Rezini. Pakamatha zaka 65, Efuraimu adzakhala ataphwanyidwaphwanyidwa moti sadzakhalanso mtundu wa anthu.+