Salimo 80:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nthambi zake zinakafika mpaka kunyanja,Ndipo mphukira zake zinafika ku Mtsinje.*+